Kwa omwe angafune kuphunzira kupanga zinthu izi; ✓Cooking oil ✓Condensed milk ✓Washing powder ✓Bar soap ✓Dish wash liquid ✓Maheu and ✓Milo Ndili ndi class lero kuyambira 4pm. Charge is K500 only. Kwa omwe mukufuna kuphunzira with that fee ponyani ma numbers mupangidwa add ku group. Thanks
$500