K U M I D I M A ( GAWO KHUMI MCHIWIRI ) 12 . “ Eyatu mwana wanga nde osamangopusitsika ndi zithu zopanda pake. “ adayankhura amayi ake a Nyadani akugoneka mutu wawo pansi. . “ Amayi ndikhulupilileni anthu awa okha ndi a chowonadi. “ . “ Popeza wakamila mwana wanga. Chabwino tipita madzurowo. “ . Nyadani pamene adangotsiliza kucheza ndi amayi ake… More

seller's name'
Name: Tsoba
seller phone number
Location: Malawi
uploaded on
Date: 04 April, 2021

Contact Seller

Loading recommendations...