A chuma amaudido ndi ochuka ambili tikalephela kupulumuka chifukwa chokonda za mziko anthu ena akakhala a chuma amalephela kuonesa chikondi kwa munthu mzao chisazo muthu osauka akhoza kukhulupilika pa maso Pao momwe iwo akufunila koma kuti iwo amuonesele chikondi momwe zimafunikila sakwanisa muthu wa udindo chimozi mozi kuti akhale pa udindo thawi… More