Ngati mphenvu zikukuvutitsani koma malo anu ndi a busy oti simungaimitse business yanu kupopera mankhwala tipezeni ife tili ndi Cockroach jelly 80gms container K28,500. Mankhwalawa ndi onukhira bwino ndipo alibe chiopsyezo kwa anthu, mankhwalawa amenewa timangopaka malo momwe zikupezeka mphenvuzo ndipo zimabwera kuzadya kenako kumafa. Imbani or WhatsApp on 0992768513, tili ku area 25C Lilongwe.