Dyna iyi muli 11B engine ya dry ndi gearbox ndi first paint tipaseni 8.5 million zinazo kumavana katundu ataonedwa pa ground tiyankhuleni 0994369880.
$8