Nissan xtrail iyi yosagwilapo engine ndi gearbox nde ndiyasmart tangoiponya mtengo wa February coz pakufunika ndalama yachangu tipaseni 12.8 million zinazo kumavana pa ground katundu ataonedwa tiyankhuleni 0994369880.
$12