Ndikugulisa Samsung tv 37" Vuto ndilakuti ikuwonekera mkati ukaiunika ndikufuna 100 mukakomzetsa nokha imbani 0885348668 muzatenge
MWK100