Plot iyi ipite moyo unsaleable pa mtengo wokambilana K 19.million .Pali mnyumba ziwiri,,ina ndiya makomo awiri ,,inayo Khomo limodxi.Madzi alipafupi ,,magetsi mapole afika kale.Very smart houses .Kuchoka bypass mtunda wa 1.km muli pa plot. Ndiyimbileni pa 0998565384/0881406204
MWK19