Zatengeni unfinished very big house iyi, three bedrooms self contained design ilinso ndi space yaikuru kwambiri. Madzi ndi magetsi zili pafupi pompo. Plaster ndi floor mumalizisa nokha ndalama imufunika mwachangu. Price K8.5 million, Ili ku Chirimba kwa Suya. For viewing call/whatsapp 0993486209 0883859204.
FREE