Looking for a plot around area 25 or nearest location Plot yake ikhoza kukhala yoti palibe kalikonse koma ikhale yaikulu 30 by 60 or above that Malo ake akhalenso pafupi ndi nyumba pofikika ndi galimoto Open budget ngat ilipo ndiyankhulen 0985225749
$10