Company ya Yellow Africa ikupitilizabe kugulitsa ma phone pangongole ! Kwa Amene sangakwanitse kugura smartphone ya new one pa cash , mwayi ulipo oti mutha kugura phone pangongole, Ma phone omwe amaperekedwa pa ngongole ndi a Tecno ndi Itel basi ndipo ma phone wa amakhara ndi warranty ya miyezi 13.. Ngongoleyi ndi ya wina aliyese Amene Ali More
FREE