Katunduyu Ali ndi engine ya new new , ndikumutaitsa pa mtengo wa ziii 680,000 No mavuto ayi chilichose chimagwila ntchito ngati Ma indicator Nyale Horn Dashboard Ma teyala nde ndamene ndakuonetsaniwo kale ilibe milanduso ayi Bweletsani makobiliwo pa mvera trading center (DOWA) DELIVERY is possible upon agreement Call 0993686474 Pictures taken Thursday/ September 12 - 2024 around 10Am No agent involved
MWK680,000