iyi ndiye yagwa mtengo sumsung galaxy S22 plus water proof phone timatsuka ngati mbale iyi camera 108MP mbambande battery limalimba kwambiri no crack chilichonse chili nchimake storage ndi 128GB headsets ndi charger zili padera contacts 0998232425/0888232425 serious buyers only sitikugulitsira desperation ayi koma tili mu nyengo ya ma Iphone sumsung apite iphone atsale
MWK895,000