*Organic hair food* ndimafuta amene amathandiza mavuto onse okhudza tsitsi..kuyabwa scarp,kuthothoka kwa tsitsi kapena ndevu,kufiila kwa tsitsi,tsitsi kusamela mmbali mbali komaso pankhongo.Tsitsi limakula mwathanzi,kubiliwila,limada,limasia kuthothoka,mmutu simumayabwa,kuthesa mfundu....natural, locks and relaxed hair..mwana,mayi komaso abambo aliyese amatha kugwilitsa ntchito.. available in, Lilongwe koma kuli konse matumiza...0991502971/drop your # nkupangen add Ku group
$2,500