Ineyo nde ndimanena always kuti katundu wabho amakhala kuno dzatengeni desktop iyi i3 20 inch monitor 350 gb HDD 4 gb ram 3.85 processor Keyboard Mouse Mukachedwa simumupeza
MWK240