Ndikugulitsa solid state Disk 128GB ,2.5 data 6GB ya desktop computer Kwamene akufuna kuwonjera ma GB Ku computer andipeze kunambala iyi Mtengo ndi 30 thousand Malawi kwacha ndipo amene angagule awiri adzapasidwa discount +265986682118 Ndimakhalira pa Ntcheu Boma Kutali ndi matumiza katundu
$30