Mukamaliza kugula zinazo mudziwe kuti pali Phone ya no madando, yoti simudandaula ndi MK85, 000 yokha, mutenga Huawei Honor 9lite, wa chi-space cha 32gb komaso 3gb ram.. kuthamanga kuposa Ferrari.. Battery kulimba kwake kuposa chibwezi chanu.. LCD yopanda ma crack, yosalala ngati nkazi wanga. chonde zatengeni Phone mbambande yi
MWK85,000