Mitsubishi Delica Automatic + Manual Transmission yogulisa. Engine ndi gearbox zonse zabwino. Misonkho ndi Bluebook zilipo. Imayenda ilibe vuto ndi yoyenda. Ili ku Ntcheu. Mtengo K3.5 million kukambirana pa ground. WhatsApp 0999050091
$35