Security systems installation training

Mwai kwa ife tonse amene timafuna titadziwa kuika ma CCTV camera, Office/Home Alarm, Fingerprint Scanner Machine/Door Access control, Intercom systems, Gate Motor ndi zina zambiri. Maphunziro akuyamba pa 05 August 2023 kulekeza pa 30 August 2024. Maro: Kaphiri, Lilongwe. Kulembetsa: K5,000 Fizi : K60,000 Kuti mudziwe zambiri imbani pa manambala awa: 0988213678 kapena 0885213678

MWK60

seller's name'
Name: Emy B
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 30 July, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0988213678
seller phone number Phone Number: 0885213678
Loading recommendations...