Ford Half Tonne yogulisa. Engine ili pa ntunda mukamanga nokha. F8 ya carburetor. Inamasulidwa imadya oil nde sinamangidweso. Ikugulisidwa mmene ilili. Ili ku Ntcheu Boma. Mtengo K1.3 million kukambirana pa ground. WhatsApp 0999050091
$130