Jmc vigus 2017 Engen TDCi 2.4L Diesel Manual Fresh in and out K15 Million no discount. Mangochi Call:0991398682/0886419383 Model iyi imayendelana chilichonse ndi ford ranger, musade nkhawa kapena kudandaula za ma Spares umu mumalowa a ford ranger. Wamwayi azapeze galimoto ya bwino pa mtengo wotsika 15 Million..
MWK15