Ma spiker aja ndangogwesa ntengo amaimba bho good for studio alibe amp ,wachangu azatenge 85pin. Sunking solar ya ma bulb awili ndungofunapo 65 last 60 yama bulb 5 pot 150 munalephela kupeleka 135 munkapempha ija zatengeni No madando kugula kumakangounikila mafon kumakango charja wagulawagula awa siomalipila pa week ai. Amp yosaika flash tima original ta jonz ta powerful tija @37k Call on 0991946788 Lilongwe area 25 nsungwi
FREE