Mercedes Benz C 200 yogulisa. Engine sinamasulidwepo. Ndi ya manual. Ofunika ku penta. Leather, mipando. Misonkho yakutha. Bluebook palibe. 1989 Model : 2.0cc Petrol Engine. Ndiyoyenda . Yopanda mavuto. Kuliza wautali. Manual gears. Misonkho yakutha. Ili ku Ntcheu. More
$95