Tipezeni ife @Achinyamata Ozitsata tikupangireni ma window,zitseko ,ma gates olimba komanso a design yapamwamba pamtengo wabwino. - Timapezekera ku Blantyre Machinjiri. -Muntha kutipeza poyimba phone kapena kutumiza uthenga pa number iyi 0888328007. -NOTE: Distance is not a barrier timapita kulikonse if transport is provided
$63