Nyumba ya rent ili ku area 49 Dubai Lilongwe Nyumbayi ili ndi two bedrooms, sitting room ndi stores Nyumbayi ili ku mpanda Madzi ndi magetsi zilipo Mtengo pa mwezi ndi 75.000 Ngati mukufuna kudzawona kapena kudziwa zambiri mutha kuyimba pa 0992335517/0885837201
FREE