Nawu Uthenga osangalatsa kuchokera ku EASI Seeds Ltd, titanva kudandaula Kwa alimi otsogola, ife a EASI Seeds takubwereserani mbeu za CABBAGE wa HYBRID wa mitundu yosiyanasiyana, CABBAGE othandiza alimi kupeza phindu, wa mkulu bwino, olemera bwino, okucha nsanga komaso olimba ku matenda. Osaiwalaso kuti mbeu za EASI seeds zimakhala ndika MTENGA konverera kuti mlimi wina aliyese athe kugula. Mukafuna kudziwa zambiri tipeze pa manambala awa 0997958140/0888037528.
FREE