Tikugulitsa ma battery a solar japan standard pantengo wazii inu kumaonera tv.choimba.kumetera pa barbershop.kuunikila.kuika pa solar irrigating pumps.nduzina zambiri zofuna mphanvu ya magetsi.tilinao new ones mukayamba nokha anzanu akugula nkumatsangalala no madando.mabattery athu onse ndiogwirabwino ntchito chifukwa pokatenga ku ware house amayetsedwa kut akhale ali pa standard.tili ku bangwe pafupi ndi police roadblock zaguleni lanu lero ndipo muzakondwa 0888909491.0992269666
$70