Farm for sale

Tili ndi farm ya mbali mwa tsinje wa shire pa zalewa 8 ectors muli kale zipatso zosiyanasiyana pamalo pofika galimoto ndinsewu waukulu pa zalewa roadbrock ma papers onse alipo mtengo 27million basi 0887778327 anafe zammafarm simbali yathu ndalama tilinazo zochita zina

MWK27

seller's name'
Name: Malawi c
seller phone number
Location: Zalewa
uploaded on
Date: 31 March, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0887778327