Plot ya bwino ikugulisidwa pa mtengo wa 2.4 Milion pa flat posafuna landscape pofika galimoto magetsi madzi zonse ziri pafupi kwambiri. Size ndi 19 by 19. Pali kale foundation ya boys quarter. For more information contact us on 0993720167.
$2,400,000