Ndikugulitsa ma rim a 15" ngati set yama rims anayi. Ndinso ma headlamps a Nissan Hardbody ngati set ya ziwiri. Ka mtengo kake ndipang'ono basi. Ndikufunapo 60 pin pa set yama rims. Ndiponso, 120 pin ma Headlamp onse awiriwa ngati set. Omwe angazikonde zinthuzi atha kundiyimbira kapena wap nambala iyi: 0995003161
MK120,000