Guzani - Inno build Plots site, tinakumbako chitsime cha hand dug, paja ndimanena mobweleza bweleza kuti ife ndife akatswiri pa ntchito yokumba zitsime za manual koma zokhala ndi water yield yomwe ingathe kupanga support any type of water pump opanda kupereka ma issues oti madzi akumatha pachitsime. Dzulo tapanga install Solar powered pump koma More
FREE