450 hectors farm ikugulitsidwa ku Mchinji ku Chimwamkango Senior Chief Mkanda. 300 hector ndi dambo pamene 150 hector ndi ku mtunda. Kwa ofuna ulimi wa mthilira kuphatikizapo mpunga komaso ziweto ndizotheka. Pamene kumtundako mbeu ina iriyonse ndi yotheka kuilima. Mtengo ndi MK750,000/hector. Call/WhatsApp 0996900111/0888996755.
FREE