*Farm for sale *Location Blantyre lirangwe *Kwa anthu omwe mumafuna kutsegula farm ndmeneyi mudzachita kutopa nayo nokha kaya ulimi wathilira ndzotheka cz malowa alipafupi nd tsinje 100 meters kuchokela mutsinje kufika pamalopa ma pipe ochepa madz osaphwera , kuchoka mu tarmac road kufka kumaloko nd 500 meters *Good access for the road *Size:8 acres *Price:13.5 negotiate *For more information u can call/wapp 0985538151
MK13