Ma ganazi ,mufuna malo abwino omangapo nyumba? Star ways yakubwereselan ma plots kawawa Ku nkholongo ma 15by30 only Pa k850,000 cash by installments its k950,000 kuyamba ndi half inayo kuimaliza Pa miyezi itatu yamphumphu komanso alipafupi ndi madzi,magesi komanso paliso madimba abwino osakana zomela tiimbilen pama nambala awa kuno kumzuzu;0984947445/0897075194 koma musatchedwe asalapo owelengeka
$850,000