Solar Security light

Pezan nawo nyal za panja zomwe ndizamakono, Nyalizo sizilira chingwe chamageai kut ziyake chifukwa zimayendera mphamvu za ya dzuwa, Zili ndi ukadaolo oziyasa zokha pamene kwada ndikuzizimisa pamene kwacha, Kumbal ya madzi ndi fumbi, nyalizi zinasekedwa bwino ndikutetezedwa ku zoterezi kut zisalowe Pa ubwino wina wa nyalizi ndiokut mutha kuika ku farm kaya pa khomo kut izikuziwisan pamene padusa chithu kapena munthu. Pofuna kuziwa zambiri imban pa number iyi 0884963362

MK34,000

seller's name'
Name: BUYING A
seller phone number
Location: Mandala, Blantyre, Malawi
uploaded on
Date: 16 January, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0884963362