Pali katundu otsika mtengo apa. Laptop mukuionayi ndi hp notebook 650. Ram 4gb HDD 300gb Battery 2 hours + Charger chake chinapoila mukagula nokha Charging base chinapoilaso ngat ndingqkhonzetse mundipasa 95 koma ngat mukakhozetsa nokhabmundipasa 83 pin. Key board imaworker bhobho kupatula + ndi Delete. For more information ndihalen oa 0990742026. Mutha kuimba or Whatsapp. Ndimakhala kuchimwankhunda. Pakufunika ndalama ya fast. Charger Chopoilacho chilipo mutha kuzatenga
$95