Nyumba ya rent ili ku area 50 lilongwe Nyumbayi ili ndi two bedroom, sitting room, dinning room, kitchen stores Madzi ndi magetsi zonse zilipo kale Nyumbayi ndi semitached Mtengo pa mwezi ndi K60.000 Nyumbayi ili ku mpanda Ngati mukufuna kudziwa zambiri ndiyimbireni pa0992335517
FREE