Malo abwino mmbali mwa njira ku area 25, Pheleni pafupifupi 800 metres kumtunda kwa Rugby stadium. Lankhulani ndi eni ake direct osati agent. Inu ofuna malo chitani machawi ndithu muwakonda malowa. Anzanu More
$3