Pa moyo wanthu pamafunika Kupeza njira zambiri zopangira ndalama kuti munthu uchite bwino pa moyo. If you are a youth or a young adults komaso umakhala ku mzuzu kuli mwayi ophuzira business mwaulele. Akupangisa ndi abugwe la Xpaging Malawi. Sunday 3rd September 2023 St John's of God hall Time :1:30 - 4:pm NOTE : Call or Whatsapp 0991512442 / 0882858185 Malo ndiochepa so do fast only 30 seats remain
FREE