MALO ogulitsa ku Blantyre kulunzu kukula kwake ndi 54 by 62 meters, magesi alipomwepo, madzinso alipmwepo, msewu ulipo, kuchoka mumsewu watala wa m1 ndi 50 meters, mtengo ndi 12 million kwacha, kukambilana kulipo ndife amalawian osadandaula, simuvutika ndizambiri ubwino wa malowa, magesi madzi ziripo, otsala pafupi koma ziripompo, numbers 0999111635 call or Whatsapp, 0888651347 call only. MALO ake ndi awa
FREE