NYUMBA YOGULITSA KWA BVUMBWE PA MTENGO WABWINO 3.5 MILLION, MAKULIDWE AKE 8AND HALF BY 530M, ZIPINDA 4. MAGESI ALI PAFUPI MAPOLO AWIRI OKHA BASI, NSINJE ULI PAFUPITSO, NSEWU WAFIKA MPAKA PAKHOMO, CHIPATALA CHILI PAFUPISO 10MINUS TAFIKA, SCHOOL ZIWIRI ZA PRIMARY ZILI PAFUPISO 10MINUS TAFIKA M,JIGO WA MADZI PAFUPI KWABASI
MK3