Kwa onse omwe amakhala ndi vuto lothobwedwa m'maso akamayendetsa galimoto usiku chifukwa cha full lights, kwabwera magalasi othandiza kuti mudziona bwino usiku poyendetsa galimoto lanu. -Mutha kuvala pamwamba pa ma galasi anu a maso omwe mumavala -Magalasiwa ndi a high definitin Mtengo ndi Mk10,000 Call or whatsapp 0999295278/088111585
$10