Mwaswela bwanji ma customer kulikonse muliko. Timagulitsa ma brand new plasma TV, pali ma size osiyanasiyana amene mungawapeze kwa ife. Tikupezekela mu Town ya Lilongwe , ku Area 1 , kuja kumagulitsidwa Matabwa kapena kuti ku. Devil Street. Dziwani za mitengo yathu ya katundu: 24" LED TV Mk 90,000 29" LED TV Mk 125,000 30" LED TV Mk 135,000 32" See more
MK165,000