Mmawa wabwino ma customer athu. Holiday ndiye yayamba iyi,kodi mwapeza plasma led tv yoti izikupatsani chimwemwe ndi zinthuzi zake zapamwamba. Timagulitsa ma brand new plasma TV ama sizes ngati 24", 30", 32" , 42",50", 55" ndi 70".
MK165,000