Nyumba yogulitsa ku area 50 lilongwe ili ku njanje ku

Nyumbayi ili ndi two bedroom, sitting room, dining room, kitchen, stores Madzi alipo kale pole lamagetsi lilipafupi kwambiri Komanso pali shop yayikulu ndimalo abusiness ndikutero chifukwa ali pa four ways Mtengo ndi 10 million kukambirana kulipo Phone number yanga ndi iyi:0992335517/0885837201

FREE

seller's name'
Name: Chingwalungwalu
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 14 December, 2022

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 2
product image 1
Image 2 of 2
Loading recommendations...