MAZDA BONGO bus yogulitsa mu Lilongwe,Likuni,,F8,manual,,misonkho yonse ilipo,,engine and gearbox intact,,yayenda pa msewu kunyamula anthu kwa myezi 5 Koma pano ili kumpanda ,mtengo 4.7 million. 0999392424 Wap and calls 0997836599/0888220085 calls only. Tsopano yatsika mtengo,,inbox.
$4