Bluetooth Adapter. Ngati muli ndi radio yoti ilibe bluetooth bola ingokhara ndi bowo la aux / input, katunduyu amapereka bluetooth ku radio yotereyi. Mukhoza kumasewera nyimbo mufoni pogwiritsa ntchito bluetooth. Zintchito zina zoonjezera zomwe katunduyu amachitanso zili muzithunzimo. Akugulitsidwa pa mtengo wa K5500
Contact seller