Malo ogulitsa ku area 50 lilongwe pali nyumba yosatha ilikufupi
Madzi ndi magetsi zili pafupi kwambiri Nyumbayi ili three bedroom, sittingroom, dining, stores , kitchen, two bathroom ndi two toilet Komanso mseu unafikapo Phone number yanga :0992335517/0885837201