Tikufuna anthu age 18 to 27 omwe angakonde kumphunzira ntchito zamanja monga carpentry, welding and plumbing. Omwe muli ndi abale anu omwe akufuna kumphunzira ntchito ngati izi kuno Ku Lilongwe aimbe number izi 0882129142/0982305817/0884725522 malo alipo ka mtengo pang'ono
$1