Mwaiwanu ogula nyumba kudera lanu lokondedwa majiga1 In Balaka Malawi wafika nyumbayi ndiya semidetached ilindi zipinda zitatu mbali Zonse ndipo magetsi metre yakeyake mbali Zonse kuli masters bedroom with ceiling palty tiled shared bathrooms and toilet mbalizonse alendi amalipra k75000 ikupata pa k25million kukambirana kulipo
$25